Episcopal Conference of Malawi

Loading

DEATH ANNOUNCEMENT

DEATH ANNOUNCEMENT

ECM Logo6th January 2016

DEATH ANNOUNCEMENT

The Catholic Secretariat of the Episcopal Conference of Malawi regrets to announce the death of Fr. Rodrick Zinyongo of Dedza Diocese. Fr. Zinyongo has passed away today, 6th January 2016 at Kamuzu Central Hospital in Lilongwe. Burial Mass will be on Friday, 8th January 2016 at Bembeke Cathedral starting from 10.00 am.

Fr. Zinyongo was ordained priest in 1984.

May the soul of Fr. Zinyongo Rest in Peace!

Rev. Fr. Henry Saindi
SECRETARY GENERAL
…………………………………………………………………………………………………

6th January, 2016

KULENGEZA UTHENGA WACHISONI

A ku likulu la Mpingo wakatolika akulengeza za imfa ya BAMBO RODRICK ZINYONGO a Dayosizi ya Dedza. Bambo Zinyongo amwalira lero pa 6 January 2016 ku chipatala chachikulu cha Kamuzu Central ku Lilongwe.

Mwambo wa Misa ya Maliro udzachitikira ku Bembeke Cathedral Lachisanu pa 8 January, 2016 kuyambira nthawi ya 10:00 mmawa.

Bambo Rodrick Zinyongo anadzozedwa unsembe m’chaka cha 1984.

Mzimu wa Bambo Zinyongo uuse ndi mtendere!

Bambo Henry Saindi
MLEMBI WAMKULU WA BUNGWE LA AEPISKOPI

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

× How can we help you?