Uthenga Ochokera kwa a Papa pa tsiku lokumbukira anthu odwala – 11 February, 2012)
‘Nyamuka, pita. Chikhulupiliro chako chakuchiritsa’ (Lk 17:19)
Okondedwa abale ndi alongo,
Pa tsiku lokumbukira anthu odwala lomwe lagwa pa tsiku la 11 February, 2012, lomwenso … Read the rest